Maerewa akhazikitsidwa lachitatu pa 21 may 2025 pamene wailesiyi yamaliza zokambilana zake ndi kampani yochititsa maere ya Supa win Malingana ndi yemwe …
Uncategorized
-
-
Uncategorized
Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.
Poyankhula Nardin Kamba bwanamkubwa wa boma la Chikwawa wapempha aphunzitsi kuti azilimbikira ntchito yawo poti boma likuyetsetsa kuwaganizira pofuna kukwaniritsa masomphenya a …
-
Uncategorized
Bungwe la center for human rights, Education,Advice and Assistance (CHREAA) lalangiza ophinzila achitsikana kuti azinena za nkhanza zogonana zomwe amakumanazo kwa adindo.
wanena izi ndi modzi mwa akuluakulu ku bungweli,mayi Hope Gee Williams pa mwambo olimbikitsa ufulu wa anthu,womwe unachitikila pa sukulu ya sekondale …
-
Ogwira ntchito komanso odwala pa chipatala cha Makhuwira adandaula kuti amavutika ndi madzi omwe amasefukira mu Mtsinje wa Thelhiwani ponena kuti amasokoneza …
-
Uncategorized
Bungwe la Maziko a Moyo Wabwino wa Onse (MAWO) lalimbikisa ntchito yosamalila zachilengedwe m’sukulu za pulayimare ndi sekondare za m’boma la chikwawa.
Wachiwiri kwa mkulu wa bungweli, a Dorothy Kamtiza ati bungweli likugwira ntchito yosamalira zomera ndi nthaka komanso kubzala mbewu zakudimba ku sukulu …
-
Uncategorized
Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe.
Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe m’dera la zamaphunziro …
-
Mafumu kwa Mfumu yaikulu Mulilima m’boma la Chikwawa athokoza Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Joyce Mtila Banda kamba kopereka chakudya kwa …
-
Uncategorized
SUKULU YOMWE UTUMIKI WA TIRDEM IKUMANGA IDZATCHULIDWA DZINA LOTI GUARDIAN CHRISTIAN ACADEMY
Utumiki wa Time of Repenting and Deliverance ku Domasi ukumanga sukulu ya Sekondare m’mudzi mwa Senior Group Namira mfumu yaikulu Mulilima ku …
-
#Nyungwe_FM_Nkhani Kwa Ngabu m’boma la Chikwawa, apolisi ati amanga mayi ena a zaka 27 kamba kotayira mwana wobereka wokha m’chimbudzi chokumba kamba …
-
Uncategorized
Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17 March 2025.
#Nyungwe_FM_Nkhani Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17 …