Home Uncategorized TRACK YATSEKA MSEWU PA KAMUZU BRIDGE BOMA LA CHIKWAWA

TRACK YATSEKA MSEWU PA KAMUZU BRIDGE BOMA LA CHIKWAWA

by Robert Malenga
0 comments

#Nyungwe_FM_Nkhani

Galimoto yonyamula katundu ya mtundu wa track panopa, yatseka msewu pa chipata cha malo ochitira chipikiseni cha apolisi pa Kamuzu Bridge m’boma la Chikwawa.

Woyendetsa galimotoyo a Ganert Nyirenda, wauza Nyungwe FM kuti ngoziyi yachitika galimotoyi italephera kukwera mtunda kamba kusokonekera kwa magiya zomwe zinachititsa kuti ibwerere m’mbuyo.

Galimototoyi yomwe nambala yake ndi NE4410 inanyamula matumba 600 a simenti yomwe imachokera ku Blantyre ndi kukatula kwa Ngabu.

Wolemba: Francis Mwale

#Liwu_la_Mchigwa

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00