M’busa wamkulu wa mpingowu, Mtumwi Albert Mpende wati mpingowu wachita izi pozindikira kuti mbewu za alimi ambiri zidapserera kamba ka ng’amba zomwe zadzetsa njala maka madera a m’boma la Chikwawa.
Pemenepa, iwo apempha amayiwa kuti asagulitse mbewuzi koma akabzale kuti akazakolola adzthe kupeza chakudya chokwanila pa banja pawo
Wolemba: Chifundo Bwalamba