Nyungwe FM
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • Nyungwe FM

    Wailesi ya Nyungwe yakhazikitsa maere omwe pakutha pa tsiku anthu oposera makumi atatu azikhala akuchita mphumi yopambana ndalama yosachepera 10,000 kwacha

    Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.

    Bungwe la center for human rights, Education,Advice and Assistance (CHREAA) lalangiza ophinzila achitsikana kuti azinena za nkhanza zogonana zomwe amakumanazo kwa adindo.

    Wailesi ya Nyungwe yakhazikitsa maere omwe pakutha pa tsiku anthu oposera makumi atatu azikhala akuchita mphumi yopambana ndalama yosachepera 10,000 kwacha

    Robert MalengaMay 22, 20250165 views

    Maerewa akhazikitsidwa lachitatu pa 21 may 2025 pamene wailesiyi yamaliza zokambilana zake ndi kampani yochititsa maere ya Supa win Malingana ndi yemwe…

    Read more

    Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.

    Robert MalengaMay 22, 20250124 views

    Poyankhula Nardin Kamba bwanamkubwa wa boma la Chikwawa wapempha aphunzitsi kuti azilimbikira ntchito yawo poti boma likuyetsetsa kuwaganizira pofuna kukwaniritsa masomphenya a…

    Read more

    Bungwe la center for human rights, Education,Advice and Assistance (CHREAA) lalangiza ophinzila achitsikana kuti azinena za nkhanza zogonana zomwe amakumanazo kwa adindo.

    Robert MalengaMay 10, 20250246 views

    wanena izi ndi modzi mwa akuluakulu ku bungweli,mayi Hope Gee Williams pa mwambo olimbikitsa ufulu wa anthu,womwe unachitikila pa sukulu ya sekondale…

    Read more

    UNITRANS YAKHAZIKITA NJIRA ZOPEWERA NGOZI

    Robert MalengaApril 25, 20250196 views

    Akuluakulu a Kampani ya UNITRANS achenjeza anthu kuti azikhala a tcheru pamene galimoto zawo zikuluzikulu zonyamula mzimbe zikudutsa m’misewu m’madera awo pofuna…

    Read more

    UTM NDI YAMPHAMVU KU CHIGWA CHA SHIRE

    Robert MalengaApril 14, 20250295 views

    Yemwe akuyimira chipani cha UTM ngati Phungu wa Nyumba ya Malamulo pakati Boma la Chikwawa pa chisankho cha pa 16 September pano,…

    Read more

    Magulu a alimi mzimbe a Kasinthula Can Growers Association m’boma la Chikwawa, pa 10 Epulo 2025 asankha Amade Alide kukhala wapampando wa alimiwa.

    Robert MalengaApril 12, 20250262 views

    Alimi a mzimbe okwana 762 ndi omwe atenga nawo mbali pa chisankhochi chomwe chinachitikira ku maofesi a zaulimi a Kasinthula pa msonkhano…

    Read more

    Mpingo wa Time of Repenting and Deliverance Ministries (TIRDEM),wapereka mbewu ya chimanga kwa amayi amasiye ndi okalamba

    Robert MalengaApril 11, 20250238 views

    M’busa wamkulu wa mpingowu, Mtumwi Albert Mpende wati mpingowu wachita izi pozindikira kuti mbewu za alimi ambiri zidapserera kamba ka ng’amba zomwe…

    Read more

    NZIKA ZACHITA ZOKAMBIRANA NDI ACHITETEZO

    Robert MalengaApril 7, 20250310 views

    Gulu la Dyeratu Nzika Lachisanu lidayitanitsa magulu a chitetezo chakumudzi a Community Policing Forum (CPF) pa zokambirana pa sukulu ya pulayimare ya…

    Read more

    CHIPATALA CHA MAKHUWIRA CHILI PA CHIOPSEZO CHA MADZI OSEFUKIRA

    Robert MalengaApril 4, 20250232 views

    Ogwira ntchito komanso odwala pa chipatala cha Makhuwira adandaula kuti amavutika ndi madzi omwe amasefukira mu Mtsinje wa Thelhiwani ponena kuti amasokoneza…

    Read more

    Bungwe la Maziko a Moyo Wabwino wa Onse (MAWO) lalimbikisa ntchito yosamalila zachilengedwe m’sukulu za pulayimare ndi sekondare za m’boma la chikwawa.

    Robert MalengaMarch 31, 20250275 views

    Wachiwiri kwa mkulu wa bungweli, a Dorothy Kamtiza ati bungweli likugwira ntchito yosamalira zomera ndi nthaka komanso kubzala mbewu zakudimba ku sukulu…

    Read more

    Posts navigation

    1 2
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top