Mlangizi wa Zamaphunziro ku zone ya Boma m’boma la Chikwawa a Tobias Tembo ayamikira zomwe bungwe la Dyeratu Nzika lachita popereka mayunifolomu kwa ophunzira pa sukulu ya pulayimare ya Dyeratu m’bomali.
Nyungwe_FM_Nkhani Poyankhula ku m’mawa wa Lolemba pa 17 March 2025 pa mwambo wopereka zovalazi, a Tembo apempha ophunzirawa kuti azigwiritse ntchito pa…