Poyankhula Nardin Kamba bwanamkubwa wa boma la Chikwawa wapempha aphunzitsi kuti azilimbikira ntchito yawo poti boma likuyetsetsa kuwaganizira pofuna kukwaniritsa masomphenya a dziko Malawi 2063.
Nawo a Gertrude Jumbe mkulu wa zamaphunziro m’bomali wagwirizana ndi pempho la bwanamkubwayu.
Naye Madalitso Nansolola ndi m’modzi mwa aphunzitsi a amayi yemwe wakwezedwa .
Iye wathokoza boma chifukwa ichi ati ndi chilimbik