Nyungwe FM
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • Nyungwe FM

    Wailesi ya Nyungwe yakhazikitsa maere omwe pakutha pa tsiku anthu oposera makumi atatu azikhala akuchita mphumi yopambana ndalama yosachepera 10,000 kwacha

    Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.

    Bungwe la center for human rights, Education,Advice and Assistance (CHREAA) lalangiza ophinzila achitsikana kuti azinena za nkhanza zogonana zomwe amakumanazo kwa adindo.

    Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe.

    Robert MalengaMarch 31, 20250262 views

    Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe m’dera la zamaphunziro…

    Read more

    Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso boma la malawi yamanga nyumba zomwe ndizolimbana ndikusitha kwa nyengo.

    Robert MalengaMarch 28, 20250363 views

    Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso Boma la Malawi, amanga nyumba zitatu zachitsanzo ku…

    Read more

    JOYCE BANDA WAPULUMUTSA ANTHU KU NJALA M'”BOMA LA CHIKWAWA

    Robert MalengaMarch 26, 20250294 views

    Mafumu kwa Mfumu yaikulu Mulilima m’boma la Chikwawa athokoza Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Joyce Mtila Banda kamba kopereka chakudya kwa…

    Read more

    SUKULU YOMWE UTUMIKI WA TIRDEM IKUMANGA IDZATCHULIDWA DZINA LOTI GUARDIAN CHRISTIAN ACADEMY

    Robert MalengaMarch 25, 20250229 views

    Utumiki wa Time of Repenting and Deliverance ku Domasi ukumanga sukulu ya Sekondare m’mudzi mwa Senior Group Namira mfumu yaikulu Mulilima ku…

    Read more

    AMUMANGA ATATAYIRA KHANDA M’CHIMBUDZI

    Robert MalengaMarch 24, 20250232 views

    #Nyungwe_FM_Nkhani Kwa Ngabu m’boma la Chikwawa, apolisi ati amanga mayi ena a zaka 27 kamba kotayira mwana wobereka wokha m’chimbudzi chokumba kamba…

    Read more

    Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17 March 2025.

    Robert MalengaMarch 23, 20250260 views

    #Nyungwe_FM_Nkhani Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17…

    Read more

    Mlangizi wa Zamaphunziro ku zone ya Boma m’boma la Chikwawa a Tobias Tembo ayamikira zomwe bungwe la Dyeratu Nzika lachita popereka mayunifolomu kwa ophunzira pa sukulu ya pulayimare ya Dyeratu m’bomali.

    Robert MalengaMarch 23, 20250295 views

    Nyungwe_FM_Nkhani Poyankhula ku m’mawa wa Lolemba pa 17 March 2025 pa mwambo wopereka zovalazi, a Tembo apempha ophunzirawa kuti azigwiritse ntchito pa…

    Read more

    TRACK YATSEKA MSEWU PA KAMUZU BRIDGE BOMA LA CHIKWAWA

    Robert MalengaMarch 23, 20250287 views

    #Nyungwe_FM_Nkhani Galimoto yonyamula katundu ya mtundu wa track panopa, yatseka msewu pa chipata cha malo ochitira chipikiseni cha apolisi pa Kamuzu Bridge…

    Read more

    #Nyungwe_FM_Nkhani

    Robert MalengaMarch 22, 20250331 views

    Gulu la Dyeratu Nzika, Lachisanu pa 21 March 2025 lalandira maphunziro olimbikitsa nzika kutengapo mbali ndi kutsatira ndondomeko za zitukuko pa Khonsolo.…

    Read more

    SUKULU YA DYERATU ILI PA VUTO LA MADZI

    Robert MalengaMarch 21, 20250291 views

    Mphunzitsi wamkulu pa sukulu ya pulayimare ya Dyeratu m’boma la Chikwawa, a Dackford Jeremia ati sukuluyi ili pa vuto lopeza madzi aukhondo…

    Read more

    Posts navigation

    1 2
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top