Bungwe la Maziko a Moyo Wabwino wa Onse (MAWO) lalimbikisa ntchito yosamalila zachilengedwe m’sukulu za pulayimare ndi sekondare za m’boma la chikwawa.
Wachiwiri kwa mkulu wa bungweli, a Dorothy Kamtiza ati bungweli likugwira ntchito yosamalira zomera ndi nthaka komanso kubzala mbewu zakudimba ku sukulu…