Wachiwiri kwa mkulu wa bungweli, a Dorothy Kamtiza ati bungweli likugwira ntchito yosamalira zomera ndi nthaka komanso kubzala mbewu zakudimba ku sukulu …
March 2025
-
-
Uncategorized
Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe.
Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe m’dera la zamaphunziro …
-
Featured
Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso boma la malawi yamanga nyumba zomwe ndizolimbana ndikusitha kwa nyengo.
Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso Boma la Malawi, amanga nyumba zitatu zachitsanzo ku …
-
Mafumu kwa Mfumu yaikulu Mulilima m’boma la Chikwawa athokoza Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Joyce Mtila Banda kamba kopereka chakudya kwa …
-
Uncategorized
SUKULU YOMWE UTUMIKI WA TIRDEM IKUMANGA IDZATCHULIDWA DZINA LOTI GUARDIAN CHRISTIAN ACADEMY
Utumiki wa Time of Repenting and Deliverance ku Domasi ukumanga sukulu ya Sekondare m’mudzi mwa Senior Group Namira mfumu yaikulu Mulilima ku …
-
#Nyungwe_FM_Nkhani Kwa Ngabu m’boma la Chikwawa, apolisi ati amanga mayi ena a zaka 27 kamba kotayira mwana wobereka wokha m’chimbudzi chokumba kamba …
-
Uncategorized
Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17 March 2025.
#Nyungwe_FM_Nkhani Ntchito yomanga malo osambira pa chipatala chaching’ono cha Chavala m’dera la Mfumu yaikulu Kasisi m’boma la Chikwawa yayamba Lolemba pa 17 …
-
Uncategorized
Mlangizi wa Zamaphunziro ku zone ya Boma m’boma la Chikwawa a Tobias Tembo ayamikira zomwe bungwe la Dyeratu Nzika lachita popereka mayunifolomu kwa ophunzira pa sukulu ya pulayimare ya Dyeratu m’bomali.
Nyungwe_FM_Nkhani Poyankhula ku m’mawa wa Lolemba pa 17 March 2025 pa mwambo wopereka zovalazi, a Tembo apempha ophunzirawa kuti azigwiritse ntchito pa …
-
#Nyungwe_FM_Nkhani Galimoto yonyamula katundu ya mtundu wa track panopa, yatseka msewu pa chipata cha malo ochitira chipikiseni cha apolisi pa Kamuzu Bridge …
-
Gulu la Dyeratu Nzika, Lachisanu pa 21 March 2025 lalandira maphunziro olimbikitsa nzika kutengapo mbali ndi kutsatira ndondomeko za zitukuko pa Khonsolo. …