Home Featured Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso boma la malawi yamanga nyumba zomwe ndizolimbana ndikusitha kwa nyengo.

Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso boma la malawi yamanga nyumba zomwe ndizolimbana ndikusitha kwa nyengo.

by Robert Malenga
0 comments

Kampani ya Illovo Sugar Malawi mogwirizana ndi bungwe la Catholic Relief Services (CRS) komanso Boma la Malawi, amanga nyumba zitatu zachitsanzo ku Nkombedzi, ku Nchalo m’boma la Chikwawa zomwe ndi zolimbana ndi kusitha kwa nyengo komanso zosalowa nthumba.

Mkulu woyang’anira ntchito ku kampani ya Illovo Sugar Malawi, a Kondwani Msimuko ati cholinga chawo ndi choti anthu azikaona nyumbazi kuti zifikire madera ena m’dziko muno.

M’mau ake Nduna yowona za Malo, a Deus Gumba ati Boma lachita chidwi ndi ntchitoyi ndipo lapanga ngwirizano ndi banki ya NBS ndi bungwe la NEEF kuti azipereka ngongole kwa Amalawi zomangira nyumba ngati izi.

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00