Maerewa akhazikitsidwa lachitatu pa 21 may 2025 pamene wailesiyi yamaliza zokambilana zake ndi kampani yochititsa maere ya Supa win Malingana ndi yemwe …
Robert Malenga
Robert Malenga
nyungwe fm is a community radio which situated in chikwawa at thabwa opposite total filling station.its goal is to educate,entertainment and inform the general public.
-
-
Uncategorized
Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.
Poyankhula Nardin Kamba bwanamkubwa wa boma la Chikwawa wapempha aphunzitsi kuti azilimbikira ntchito yawo poti boma likuyetsetsa kuwaganizira pofuna kukwaniritsa masomphenya a …
-
Uncategorized
Bungwe la center for human rights, Education,Advice and Assistance (CHREAA) lalangiza ophinzila achitsikana kuti azinena za nkhanza zogonana zomwe amakumanazo kwa adindo.
wanena izi ndi modzi mwa akuluakulu ku bungweli,mayi Hope Gee Williams pa mwambo olimbikitsa ufulu wa anthu,womwe unachitikila pa sukulu ya sekondale …
-
Akuluakulu a Kampani ya UNITRANS achenjeza anthu kuti azikhala a tcheru pamene galimoto zawo zikuluzikulu zonyamula mzimbe zikudutsa m’misewu m’madera awo pofuna …
-
Yemwe akuyimira chipani cha UTM ngati Phungu wa Nyumba ya Malamulo pakati Boma la Chikwawa pa chisankho cha pa 16 September pano, …
-
FeaturedOpinion
Magulu a alimi mzimbe a Kasinthula Can Growers Association m’boma la Chikwawa, pa 10 Epulo 2025 asankha Amade Alide kukhala wapampando wa alimiwa.
Alimi a mzimbe okwana 762 ndi omwe atenga nawo mbali pa chisankhochi chomwe chinachitikira ku maofesi a zaulimi a Kasinthula pa msonkhano …
-
Featured
Mpingo wa Time of Repenting and Deliverance Ministries (TIRDEM),wapereka mbewu ya chimanga kwa amayi amasiye ndi okalamba
M’busa wamkulu wa mpingowu, Mtumwi Albert Mpende wati mpingowu wachita izi pozindikira kuti mbewu za alimi ambiri zidapserera kamba ka ng’amba zomwe …
-
Gulu la Dyeratu Nzika Lachisanu lidayitanitsa magulu a chitetezo chakumudzi a Community Policing Forum (CPF) pa zokambirana pa sukulu ya pulayimare ya …
-
Ogwira ntchito komanso odwala pa chipatala cha Makhuwira adandaula kuti amavutika ndi madzi omwe amasefukira mu Mtsinje wa Thelhiwani ponena kuti amasokoneza …
-
Uncategorized
Bungwe la Maziko a Moyo Wabwino wa Onse (MAWO) lalimbikisa ntchito yosamalila zachilengedwe m’sukulu za pulayimare ndi sekondare za m’boma la chikwawa.
Wachiwiri kwa mkulu wa bungweli, a Dorothy Kamtiza ati bungweli likugwira ntchito yosamalira zomera ndi nthaka komanso kubzala mbewu zakudimba ku sukulu …