Home Uncategorized Wailesi ya Nyungwe yakhazikitsa maere omwe pakutha pa tsiku anthu oposera makumi atatu azikhala akuchita mphumi yopambana ndalama yosachepera 10,000 kwacha

Wailesi ya Nyungwe yakhazikitsa maere omwe pakutha pa tsiku anthu oposera makumi atatu azikhala akuchita mphumi yopambana ndalama yosachepera 10,000 kwacha

by Robert Malenga
0 comments

Maerewa akhazikitsidwa lachitatu pa 21 may 2025 pamene wailesiyi yamaliza zokambilana zake ndi kampani yochititsa maere ya Supa win

Malingana ndi yemwe akuedetsa za maelewa M’modzi mwa ogwira ntchito kuchokera pa wailesi ya Nyungwe Robert Benson Malenga wati maelewa azitchulidwa kuti Nyungwe Supa win omwe kulowa kwake ndi kuimba *4348 * 26 # pa lamya ya mmanja

Kuonjezera apo omwe akutenga mbali yochita maelewa akuenera kukhala ndi ndalama yosachepera 500 kwacha Ku mpamba kapena Airtel money yomwe iziwathandizira kugura tikiti yolowera mu maelewa ndikukhala pa ndandanda wa anthu omwe azikhala akuchita mphumi nthawi iliyonse yomwe maelewa akuchitika.

Olemba Martha Chirwa M’biza

#Liwu la M’chigwa

May be a graphic of text that says 'SUPA WIN KUSINTHA MIOYO'

All reactions:

10Moses Moyala and 9 others

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00