Home Uncategorized Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.

Boma la Malawi kudzera ku khonsolo ya boma la Chikwawa lakweza pantchito aphunzitsi a m’sukulu za pulayimale pafupifupi 900 a m’bomali.

by Robert Malenga
0 comments

Poyankhula Nardin Kamba bwanamkubwa wa boma la Chikwawa wapempha aphunzitsi kuti azilimbikira ntchito yawo poti boma likuyetsetsa kuwaganizira pofuna kukwaniritsa masomphenya a dziko Malawi 2063.

Nawo a Gertrude Jumbe mkulu wa zamaphunziro m’bomali wagwirizana ndi pempho la bwanamkubwayu.

Naye Madalitso Nansolola ndi m’modzi mwa aphunzitsi a amayi yemwe wakwezedwa .

Iye wathokoza boma chifukwa ichi ati ndi chilimbik

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00