Home Featured Mpingo wa Time of Repenting and Deliverance Ministries (TIRDEM),wapereka mbewu ya chimanga kwa amayi amasiye ndi okalamba

Mpingo wa Time of Repenting and Deliverance Ministries (TIRDEM),wapereka mbewu ya chimanga kwa amayi amasiye ndi okalamba

by Robert Malenga
0 comments

M’busa wamkulu wa mpingowu, Mtumwi Albert Mpende wati mpingowu wachita izi pozindikira kuti mbewu za alimi ambiri zidapserera kamba ka ng’amba zomwe zadzetsa njala maka madera a m’boma la Chikwawa.

Pemenepa, iwo apempha amayiwa kuti asagulitse mbewuzi koma akabzale kuti akazakolola adzthe kupeza chakudya chokwanila pa banja pawo

Wolemba: Chifundo Bwalamba

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00