Home Uncategorized Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe.

Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe.

by Robert Malenga
0 comments

Bungwe la Community Focus (COFO) Lachitatu pa 26 March 2025 lapereka zipangizo zophunzirira pa sukulu ya pulayimare ya Matchombe m’dera la zamaphunziro la Boma m’boma la Chikwawa.

Mkulu wa bungweli, a Joshua Malunga awuza wailesi ya Nyungwe kuti apereka ma yunifolomu komanso nsapato kwa ophunzira amasiye komanso ovutikitsitsa okwana 60.

A Malunga ati aperekanso mabuku, makopo ndi zolembera ndi cholinga choti maphunziro apite patsolo m’boma la Chikwawa.

Wolemba: Chifundo Bwalamba

#Liwu_la_Mchigwa

Wojambula zithunzi: COFO

All reactions:

1414

You may also like

Leave a Comment

Nyungwe FM 107.6MHz is located near Thabwa Road Block in Chikwawa district.
Voice of the valley.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00